Thursday, February 25, 2010

Malawi's First Lady in action

Malawi's in-coming First lady Madame Calista Chapola Chimombo (right) has taken into action as wife to Malawi State President Ngwazi Dr Bingu wa Mutharika. Madame Chimombo, herself a former cabinet minister and distinguished member of the ruling Democratic Progressive Party engaged President Mutharika on 14th February( the Valentines Day), 2010.

The couple is set to get married in the Roman Catholic church on 1st May, 2010.

Waiting for her official marriage day, has not stopped the in-coming Malawi First Lady from getting into action in her new role. Over the weekend, Madame Chimombo was in the tea growing district of Thyolo, southern Malawi where she presided over the launch of a government initiative on family support package for child headed households in Thyolo East.

In the picture, looking on is Women and Children Affairs Minister, Patricia Kaliati and Justice and Constitutional Affairs Minister and Member of Parliament for the area, Professor Arthur Peter Mutharika-Malawi Digest.

12 comments:

  1. Chipongwe sichimathandiza, lero Kaliati wayamba kumugwadila nzimayi yemwe poyamba amamuchitira mwano. Kupita ku constituency yake kukamupanga decampaign, kumukaniza office mmene anasankhidwa Minister of Tourism. Lero akumugwadila lero. Iwe Kaliati, uyambe kukonda amayi anzako, do not have plastic smiles, wamva iwe Kaliati? Munthu woipa iwe, umachitira nsanje anzako

    ReplyDelete
  2. Komano a First lady mukakhazikika, musazaloleleso zomanyamulitsa ana matumba choncho.

    Zimenezi zimakhala nkhaza kwa ana, a Malawi tiyeni tisinthe nkhalidwe omanyamulitsa ana akatundu olemera choncho. Pamenepo panali pa msonkhano, ndikhulupirira kut panali anyamata achikulire oti akanatha kutumikira

    ReplyDelete
  3. Anawo amaopa kuti akuluakulu athawa nalo thumba lawolo. Koma abale ana akuzunzika ku Malawi kwathuko ndithu.

    ReplyDelete
  4. CHILD ABUSE BY MAMA CHIMOMBO

    >WHY USE YOUNG CHILDREN TO CARRY HEAVY LOADS? MAY THE AUTHORITIES LOOK INTO THIS ZOCHITISA MANYAZI.

    ReplyDelete
  5. Off course she would go ku MTL-where else has she jurisdiction-Rt Honarable Banda is all over doing an extra good job. We are all witnesses with a meagre source of resources she is still fighting for us. Way to go Rt Honarable VP

    ReplyDelete
  6. well done first lady to be.pitilizane mwina mungakhale ngati diana princess of wales..lol

    ReplyDelete
  7. mayi mukhazikike tsopano mwakwatiwa osati tizimva zoti zoti.......

    ReplyDelete
  8. Mwachita mwayi kuti amuna anu atsopano a Bingu samva za wanthu, kukhala enafe mbiri za inu mayi timamva pakatipa kuti mwayendapo ndi amuna ambiri ndipo maina anatchulidwa: tikanakusiyani.
    Ndiye langizo langa loyamba ndiloti musakaithawire nkhalamba kusata anyamata mwasankha nokha anthu tikuona ndi kumva.

    Anthu anena kuti ndinu okongola inde koma musatengeke nako kukongola, chifukwa zonse nchabe koma chikondi ndi kukhulupilika basi.

    Musakaimwetse kondaine mdalayo ayi!!!

    ReplyDelete
  9. www.malawivoice.com

    latest news from malawi

    ReplyDelete
  10. www.malawivoice.com

    ReplyDelete
  11. Mukungochita jealousy nzanutu watola chithumba. Mukhaula muona!!!!!!!!!

    ReplyDelete
  12. Zoona madam ,thats a good start

    ReplyDelete